Maliro 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Wodzozedwa wa Yehova,+ amene ndi mpweya wotuluka mphuno mwathu,+ wagwidwa m’dzenje lawo lalikulu.+Ponena za ameneyu, ife tinati: “Tidzakhala mumthunzi wake+ pakati pa mitundu ya anthu.”+ Mika 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pa tsikulo munthu adzanena mwambi+ wokhudza anthu inu ndipo ndithu adzakuimbirani nyimbo ya maliro.+ Anthu adzanena kuti: “Ife talandidwa zinthu zathu!+ Cholowa cha anthu amtundu wathu chaperekedwa kwa anthu ena.+ Talandidwa cholowa chathu. Iye wapereka minda yathu kwa anthu osakhulupirika.”
20 Wodzozedwa wa Yehova,+ amene ndi mpweya wotuluka mphuno mwathu,+ wagwidwa m’dzenje lawo lalikulu.+Ponena za ameneyu, ife tinati: “Tidzakhala mumthunzi wake+ pakati pa mitundu ya anthu.”+
4 Pa tsikulo munthu adzanena mwambi+ wokhudza anthu inu ndipo ndithu adzakuimbirani nyimbo ya maliro.+ Anthu adzanena kuti: “Ife talandidwa zinthu zathu!+ Cholowa cha anthu amtundu wathu chaperekedwa kwa anthu ena.+ Talandidwa cholowa chathu. Iye wapereka minda yathu kwa anthu osakhulupirika.”