Oweruza 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo kamtengo kamingako kanauza mitengoyo kuti, ‘Ngati mukunenadi zoona kuti mukufuna kundidzoza kuti ndikhale mfumu, bwerani mubisale mumthunzi wanga.+ Koma ngati si choncho, moto+ utuluke mwa ine ndi kunyeketsa mikungudza+ ya ku Lebanoni.’+ Danieli 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Masamba ake anali okongola ndipo unali ndi zipatso zambiri. Mumtengomo munali zakudya zokwanira chamoyo chilichonse. Nyama zakutchire+ zinali kukhala mumthunzi wake.+ Mbalame zam’mlengalenga zinali kukhala panthambi zake+ ndipo zamoyo zonse zinali kupeza chakudya mmenemo.
15 Pamenepo kamtengo kamingako kanauza mitengoyo kuti, ‘Ngati mukunenadi zoona kuti mukufuna kundidzoza kuti ndikhale mfumu, bwerani mubisale mumthunzi wanga.+ Koma ngati si choncho, moto+ utuluke mwa ine ndi kunyeketsa mikungudza+ ya ku Lebanoni.’+
12 Masamba ake anali okongola ndipo unali ndi zipatso zambiri. Mumtengomo munali zakudya zokwanira chamoyo chilichonse. Nyama zakutchire+ zinali kukhala mumthunzi wake.+ Mbalame zam’mlengalenga zinali kukhala panthambi zake+ ndipo zamoyo zonse zinali kupeza chakudya mmenemo.