Habakuku 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ine ndidzaimabe+ pamalo a mlonda ndiponso pakhoma lachitetezo. Ndidzakhala tcheru+ kuti ndione uthenga umene iye adzalankhula kudzera mwa ine+ ndi zimene ndidzayankha pamene iye akundidzudzula.+ Habakuku Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:1 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2018, ptsa. 15-16 Nsanja ya Olonda,11/15/2007, tsa. 102/1/2000, ptsa. 12, 145/15/1989, ptsa. 24-25
2 Ine ndidzaimabe+ pamalo a mlonda ndiponso pakhoma lachitetezo. Ndidzakhala tcheru+ kuti ndione uthenga umene iye adzalankhula kudzera mwa ine+ ndi zimene ndidzayankha pamene iye akundidzudzula.+
2:1 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2018, ptsa. 15-16 Nsanja ya Olonda,11/15/2007, tsa. 102/1/2000, ptsa. 12, 145/15/1989, ptsa. 24-25