March Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano March 2017 Zitsanzo za Ulaliki March 6-12 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 1-4 “Ine Ndili ndi Iwe Kuti Ndikulanditse” March 13-19 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 5-7 Anasiya Kuchita Zimene Mulungu Ankafuna MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Tingagwiritse Ntchito Bwanji Kabuku Kakuti Kodi Ndani Akuchita Chifuniro cha Yehova Masiku Ano? March 20-26 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 8-11 Anthu Akamatsogoleredwa ndi Yehova Zinthu Zimawayendera Bwino MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Tingagwiritse Ntchito Bwanji Kabuku Kakuti Mverani Mulungu? March 27–April 2 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 12-16 Aisiraeli Anaiwala Yehova MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzithandiza Banja Lanu Kuti Lizikumbukira Yehova