November Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya November 2017 Zitsanzo za Ulaliki November 6-12 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AMOSI 1-9 ‘Yesetsani Kufunafuna Yehova Kuti Mupitirize Kukhala ndi Moyo’ MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Kupanga Ulendo Wobwereza November 13-19 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | OBADIYA 1–YONA 4 Muziphunzirapo Kanthu pa Zimene Munalakwitsa MOYO WATHU WACHIKHRISTU Zimene Tikuphunzira Kuchokera m’Buku la Yona November 20-26 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MIKA 1-7 Kodi Yehova Amafuna Kuti Tizichita Chiyani? November 27–December 3 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | NAHUMU 1–HABAKUKU 3 Khalanibe Maso MOYO WATHU WACHIKHRISTU Khalanibe Maso Pamene Zinthu Zasintha