Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2014 CHIPEMBEDZO Mmene Mulungu Analengera Zinthu Zonsezi? 3/14 KUCHEZA NDI ANTHU Dokotala wa Opaleshoni (G. Perez), 5/14 Katswiri wa Chitetezo cha M’thupi (H. Kotlar), 2/14 Katswiri wa Zachuma (S. Taylor), 12/14 Katswiri Wasayansi (F. Yang), 1/14 Katswiri Wasayansi (W. He), 7/14 Katswiri Wofufuza Zamankhwala (F. Dumoulin), 4/14 KUCHITA ZINTHU NDI ANTHU Kodi Mungatani Kuti Mugwirizanenso? 8/14 Mukamatumiza Kapena Kulandira Mameseji pa Foni, 7/14 Mumatani Wina Akakupatsani Malangizo? 4/14 Mungatani Kuti Mukhale Bwenzi Labwino? 6/14 Mungatani Kuti Musamagonje Mukakumana ndi Mayesero? 10/14 Mungatani Kuti Musamangotengera Zochita za Anzanu? 1/14 Mungatani Kuti Musamasunge Chakukhosi? 9/14 Mungatani Kuti Muzilolerana M’banja? 12/14 Musamangopatsa Mwana Wanu Chilichonse, 8/14 Ngati Banja Lanu Silikuyenda Bwino, 3/14 Ngati Mwana Wanu Amanama, 11/14 Ngati Mwana Wanu Wamkazi Akuvutika Maganizo, 2/14 Phunzitsani Ana Anu Kuti Azigwiritsa Ntchito Intaneti Moyenera, 5/14 MAYIKO NDI ANTHU Belize, 10/14 Cambodia, 4/14 Dziko La Spain Linathamangitsa a Morisco, 8/14 El Salvador, 3/14 Ireland, 7/14 Italy, 1/14 Ngalande za Madzi za ku Roma, 11/14 Nyumba Yomwe Imakumbutsa Anthu za Bomba Loopsa, 11/14 MBONI ZA YEHOVA Anandithandiza pa Nthawi Yomwe Ndinkafunikiradi Kuthandizidwa (M. Aleksza), 11/14 NYAMA NDI ZOMERA Alimi Odziwa Kusamalira Nkhalango (mileme ya m’nkhalango), 10/14 Kanyama Kakang’ono ka Maso Aakulu, 12/14 “Onetsetsani Mbalame,” 8/14 SAYANSI Achule Amene Amaswa Modabwitsa Kwambiri, 7/14 Chimene Chimachititsa Kuti Dzombe Lisamawombane Pouluka, 9/14 Gulugufe wa Mapiko Odabwitsa Zedi, 8/14 Kangaude Wam’nyumba, 1/14 Khungu la Njoka, 3/14 Kuwala kwa Ziphaniphani, 2/14 Mapiko a Gulugufe, 4/14 Miyendo ya Hatchi, 10/14 Tim’guza Ndowe Timachita Zogometsa, 6/14 TIONE ZAKALE Constantine, 2/14 Joseph Priestley, 6/14 William Whiston, 8/14 UMOYO NDI MANKHWALA Kupanikizika Chifukwa cha Ntchito, 9/14 Kuvutika Maganizo, 5/14 Matenda a Chiseyeye, 6/14 Matenda a Muubongo, 12/14 Zimene Mungachite Kuti Mupewe Matenda a Shuga, 9/14 ZACHUMA NDI NTCHITO Mungatani Kuti Musamawononge Ndalama Zambiri? 6/14 ZIMENE BAIBULO LIMANENA Dziko Lapansi, 12/14 Imfa, 6/14 Kukhulupirira Mizimu, 2/14 Kulenga, 1/14 Kusankhana Mitundu, 4/14 Kusinkhasinkha, 5/14 Maloto Ochokera kwa Mulungu, 8/14 Ndalama, 3/14 Pemphero, 9/14 Ukhondo, 11/14 Zifaniziro, 10/14 Zipembedzo, 7/14 ZOSIYANASIYANA Kodi Kudzipha Ndi Njira Yabwino Yothetsera Mavuto? 4/14 Kodi Mungatani Kuti Muzisangalala? 11/14 Kufufuza Anthu Amene Ankawaganizira Kuti Ndi Mfiti, 5/14 Misozi, 3/14 Mumaonera Chiyani Kuti Munthu Zikumuyendera? 10/14 Mungatani Mutakumana Ndi Vuto Lalikulu? 7/14 Muzigwiritsa Ntchito Bwino Nthawi, 2/14 ‘Nzeru Ikufuula,’ 5/14 Webusaiti Yothandiza Kwambiri (jw.org/ny), 1/14