LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsa. 15
  • Kodi Mungatengele Bwanji Citsanzo ca Anazili?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Mungatengele Bwanji Citsanzo ca Anazili?
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Zimene Tikuphunzilapo kwa Anazili
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2024
  • Yehova Anasintha Tembelelo Kukhala Dalitso
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Utumiki wa Alevi
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Zimene Tingaphunzile pa Dongosolo la Msasa wa Aisiraeli
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 January tsa. 15

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Mungatengele Bwanji Citsanzo ca Anazili?

Anazili anali kukhala odzimana (Num. 6:2-4; it-2 477)

Anazili anali na mtima wogonjela pocita cifunilo ca Yehova (Num. 6:5)

Nthawi zonse Anazili anali kukhala oyela pamaso pa Yehova (Num. 6:6, 7)

Masiku anonso, atumiki a nthawi zonse amaonetsa mtima wodzimana komanso wogonjela kwa Yehova na makonzedwe ake.

Zithunzi: Abale na alongo akucita utumiki wanthawi zonse. 1. Abale aŵili apainiya akulalikila munthu amene ali pabulu. 2. M’bale na mlongo akugwila nchito yomanga.
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani