Cigawo 3 Yopulinta Nkhani Yake: Kuona zimene Mulungu amayembekezela kwa alambili ake MAPHUNZILO 34 Kodi Tingaonetse Bwanji Kuti Yehova Timamukonda? 35 Mmene Tingapangile Zisankho Zabwino 36 Khalani Woona Mtima pa Zinthu Zonse 37 Kodi Baibo Imakamba Ciyani pa za Nchito Komanso Ndalama? 38 Tiziiyamikila Mphatso ya Moyo 39 Mmene Mulungu Amawaonela Magazi 40 Tiyenela Kucita Ciyani Kuti Tikhale Oyela Pamaso pa Mulungu? 41 Kodi Baibo Imati Ciyani pa Nkhani ya Kugonana? 42 Kodi Baibo Imati Ciyani pa Nkhani ya Umbeta na Ukwati? 43 Kodi Nkhani ya Kumwa Moŵa Akhristu Ayenela Kuiona Bwanji? 44 Kodi Zikondwelelo Zonse Zimam’sangalatsa Mulungu? 45 Tanthauzo la Kusakhalila Mbali 46 N’cifukwa Ciyani Muyenela Kudzipatulila na Kubatizika? 47 Kodi Ndinu Wokonzeka Kubatizika?