2 Samueli 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako anaika mafupa a Sauli ndi Yonatani mwana wake m’dziko la Benjamini ku Zela+ m’manda a Kisi+ bambo ake, kuti achite zonse zimene mfumu inalamula. Izi zitachitika, Mulungu anamvetsera kuchonderera kwawo kuti amvere chisoni dziko lawo.+ 2 Mbiri 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Manase anayamba kupemphera kwa Mulungu ndipo iye anamva kupembedzera kwake+ ndi pempho lake lopempha chifundo. Kenako anam’bwezera ku Yerusalemu ku ufumu wake,+ ndipo Manase anadziwa kuti Yehova ndiye Mulungu woona.+ Luka 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mngeloyo anamuuza kuti: “Usachite mantha Zekariya, chifukwa pembedzero lako lamveka ndithu.+ Mkazi wako Elizabeti adzakuberekera mwana wamwamuna, ndipo udzamutche Yohane.+
14 Kenako anaika mafupa a Sauli ndi Yonatani mwana wake m’dziko la Benjamini ku Zela+ m’manda a Kisi+ bambo ake, kuti achite zonse zimene mfumu inalamula. Izi zitachitika, Mulungu anamvetsera kuchonderera kwawo kuti amvere chisoni dziko lawo.+
13 Manase anayamba kupemphera kwa Mulungu ndipo iye anamva kupembedzera kwake+ ndi pempho lake lopempha chifundo. Kenako anam’bwezera ku Yerusalemu ku ufumu wake,+ ndipo Manase anadziwa kuti Yehova ndiye Mulungu woona.+
13 Koma mngeloyo anamuuza kuti: “Usachite mantha Zekariya, chifukwa pembedzero lako lamveka ndithu.+ Mkazi wako Elizabeti adzakuberekera mwana wamwamuna, ndipo udzamutche Yohane.+