Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 45:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Koma atamufotokozera mawu onse amene Yosefe ananena, ndiponso ataona ngolo zimene Yosefe anatumiza kuti zidzam’tenge, mtima wa Yakobo bambo awo unayamba kubwereramo.+

  • Genesis 46:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kenako, Yakobo ananyamuka ku Beere-sebako. Ana a Isiraeliwo anatenga bambo awo, Yakobo, limodzi ndi ana awo aang’ono, ndi akazi awo. Anawatengera m’ngolo zimene Farao anatumiza.+

  • Numeri 7:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Anabweretsa zopereka zawo pamaso pa Yehova. Zoperekazo zinali ngolo 6 zotseka pamwamba, ndi ng’ombe 12. Zimenezi zikutanthauza kuti atsogoleri awiri anapereka ngolo imodzi, ndipo mtsogoleri aliyense anapereka ng’ombe yamphongo imodzi. Zoperekazo anafika nazo pachihema chopatulika.

  • 1 Samueli 6:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ngoloyo inafika m’munda wa Yoswa, amene kwawo kunali ku Beti-semesi, ndi kuima pamalo pamene panali mwala waukulu. Ndiyeno anthuwo anawaza matabwa a ngoloyo ndipo ng’ombezo+ anazipereka nsembe yopsereza kwa Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena