19 Uwauzenso kuti:+ “Chitani izi: Mutenge ngolo+ kuno ku Iguputo zokatengera ana anu aang’ono ndi akazi anu. Ngolo ina mukatengere bambo anu n’kubwera kuno.+
47Yosefe anafikadi kwa Farao n’kumuuza kuti:+ “Bambo anga ndi abale anga abwera kuchokera ku Kanani. Abwera ndi nkhosa zawo, ng’ombe zawo ndi zonse zimene ali nazo, ndipo afikira ku Goseni.”+