Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 25:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ndidziwitseni njira zanu, inu Yehova.+

      Ndiphunzitseni kuyenda m’njira zanu.+

  • Salimo 27:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndilangizeni, inu Yehova, kuti ndiyende m’njira yanu.+

      Nditsogolereni m’njira yowongoka kuti nditetezeke kwa adani anga.

  • Salimo 86:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Inu Yehova, ndilangizeni za njira yanu.+

      Ndidzayenda m’choonadi chanu.+

      Ndipatseni mtima wosagawanika kuti ndiope dzina lanu.+

  • Salimo 119:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  33 Ndilangizeni inu Yehova, kuti ndiyende motsatira malangizo anu,+

      Kuti nditsatire malangizo anu moyo wanga wonse.+

  • Yesaya 30:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Makutu ako adzamva mawu kumbuyo kwako, akuti: “Njira ndi iyi.+ Yendani mmenemu anthu inu.” Yendani m’njira imeneyi kuti musasochere n’kulowera kudzanja lamanja kapena lamanzere.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena