Ekisodo 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno Mose atakhala kumeneko nthawi yaitali, mfumu ya Iguputo inamwalira.+ Koma ana a Isiraeli anapitirizabe kuvutika ndi ukapolo ndi kulira modandaula.+ Iwo anapitirizabe kulirira thandizo kwa Mulungu woona chifukwa cha ukapolowo.+ Miyambo 14:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Wobera munthu wosauka mwachinyengo amanyoza amene anamupanga,+ koma wokomera mtima munthu wosauka amalemekeza amene anamupanga.+ Machitidwe 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo Mulungu ananenanso kuti mbewu yake idzakhala alendo+ m’dziko lachilendo,+ ndipo anthu adzawasandutsa akapolo ndi kuwasautsa kwa zaka 400.+
23 Ndiyeno Mose atakhala kumeneko nthawi yaitali, mfumu ya Iguputo inamwalira.+ Koma ana a Isiraeli anapitirizabe kuvutika ndi ukapolo ndi kulira modandaula.+ Iwo anapitirizabe kulirira thandizo kwa Mulungu woona chifukwa cha ukapolowo.+
31 Wobera munthu wosauka mwachinyengo amanyoza amene anamupanga,+ koma wokomera mtima munthu wosauka amalemekeza amene anamupanga.+
6 Ndipo Mulungu ananenanso kuti mbewu yake idzakhala alendo+ m’dziko lachilendo,+ ndipo anthu adzawasandutsa akapolo ndi kuwasautsa kwa zaka 400.+