Danieli 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamenepo Sadirake, Mesake ndi Abedinego anayankha mfumuyo kuti: “Inu mfumu Nebukadinezara, palibenso chimene ife tinganene kwa inu pa nkhani imeneyi.+ Danieli 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nthawi yomweyo iwo anauza mfumuyo kuti: “Danieli,+ mmodzi wa anthu amene anatengedwa ukapolo ku Yuda,+ sanakumvereni mfumu komanso sanamvere lamulo limene munasainira ndipo akupemphera katatu pa tsiku.”+ Mateyu 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+ Machitidwe 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Poyankha Petulo ndi atumwi enawo ananena kuti: “Ife tiyenera kumvera Mulungu monga wolamulira, osati anthu.+
16 Pamenepo Sadirake, Mesake ndi Abedinego anayankha mfumuyo kuti: “Inu mfumu Nebukadinezara, palibenso chimene ife tinganene kwa inu pa nkhani imeneyi.+
13 Nthawi yomweyo iwo anauza mfumuyo kuti: “Danieli,+ mmodzi wa anthu amene anatengedwa ukapolo ku Yuda,+ sanakumvereni mfumu komanso sanamvere lamulo limene munasainira ndipo akupemphera katatu pa tsiku.”+
28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+
29 Poyankha Petulo ndi atumwi enawo ananena kuti: “Ife tiyenera kumvera Mulungu monga wolamulira, osati anthu.+