Ekisodo 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano Yehova anauza Mose kuti: “Tambasula dzanja lako+ ndi kuloza kumwamba, kuti matalala+ agwe m’dziko lonse la Iguputo, kuti agwere anthu, nyama ndi zomera zonse m’dziko la Iguputo.” Ekisodo 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chotero Yehova anauza Mose kuti: “Tambasula+ dzanja lako ndi kuloza dziko la Iguputo, kuti dzombe ligwe m’dziko lonselo ndi kudya zomera zonse za m’dzikomo, chilichonse chimene matalala anasiya.”+ Ekisodo 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano Mose anatambasula dzanja lake kuloza panyanja,+ ndipo Yehova anachititsa mphepo yamphamvu yakum’mawa kuyamba kugawa nyanjayo usiku wonse ndi kuumitsa pansi pake.+ Motero madziwo anali kugawikana.+
22 Tsopano Yehova anauza Mose kuti: “Tambasula dzanja lako+ ndi kuloza kumwamba, kuti matalala+ agwe m’dziko lonse la Iguputo, kuti agwere anthu, nyama ndi zomera zonse m’dziko la Iguputo.”
12 Chotero Yehova anauza Mose kuti: “Tambasula+ dzanja lako ndi kuloza dziko la Iguputo, kuti dzombe ligwe m’dziko lonselo ndi kudya zomera zonse za m’dzikomo, chilichonse chimene matalala anasiya.”+
21 Tsopano Mose anatambasula dzanja lake kuloza panyanja,+ ndipo Yehova anachititsa mphepo yamphamvu yakum’mawa kuyamba kugawa nyanjayo usiku wonse ndi kuumitsa pansi pake.+ Motero madziwo anali kugawikana.+