Ekisodo 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Komabe, Farao nayenso anaitana amuna ake anzeru ndi amatsenga.+ Choncho ansembe ochita zamatsenga a ku Iguputo anachitanso zomwezo mwa matsenga awo.+ Ekisodo 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo ansembe ochita zamatsenga, anafunanso kuti apange ntchentche zoluma mwa matsenga awo,+ koma analephera.+ Ndipo ntchentchezo zinali kuluma anthu ndi nyama zomwe. 2 Timoteyo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano monga mmene Yane ndi Yambure+ anatsutsira Mose, anthu amenewanso akupitiriza kutsutsa choonadi.+ Iwo ali ndi maganizo opotoka kwambiri,+ ndipo sakuyenerera chikhulupirirochi.+
11 Komabe, Farao nayenso anaitana amuna ake anzeru ndi amatsenga.+ Choncho ansembe ochita zamatsenga a ku Iguputo anachitanso zomwezo mwa matsenga awo.+
18 Ndipo ansembe ochita zamatsenga, anafunanso kuti apange ntchentche zoluma mwa matsenga awo,+ koma analephera.+ Ndipo ntchentchezo zinali kuluma anthu ndi nyama zomwe.
8 Tsopano monga mmene Yane ndi Yambure+ anatsutsira Mose, anthu amenewanso akupitiriza kutsutsa choonadi.+ Iwo ali ndi maganizo opotoka kwambiri,+ ndipo sakuyenerera chikhulupirirochi.+