Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 7:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Komano, ansembe ochita zamatsenga a ku Iguputo anachitanso zomwezo mwa matsenga awo,+ moti Farao anaumitsabe mtima wake,+ ndipo sanamvere Mose ndi Aroni, monga Yehova ananenera.+

  • Ekisodo 8:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndipo ansembe ochita zamatsenga, anafunanso kuti apange ntchentche zoluma mwa matsenga awo,+ koma analephera.+ Ndipo ntchentchezo zinali kuluma anthu ndi nyama zomwe.

  • Ekisodo 9:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndipo ansembe ochita zamatsenga sanathe kuonekera pamaso pa Mose chifukwa cha zithupsazo, popeza zinatuluka pa ansembewo ndi pa Aiguputo onse.+

  • Machitidwe 8:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Tsopano mumzindawo munalinso munthu wina dzina lake Simoni. Izi zisanachitike, iyeyu anali kuchita zamatsenga+ ndi kudabwitsa anthu onse mu Samariya. Anali kudzitamandira kuti anali wopambana.+

  • 2 Atesalonika 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma kukhalapo kwa wosamvera malamuloyo kukutheka mwa mphamvu+ za Satana. Adzachita ntchito iliyonse yamphamvu ndi zizindikiro zabodza ndi zodabwitsa,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena