Ekisodo 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Komabe, Farao nayenso anaitana amuna ake anzeru ndi amatsenga.+ Choncho ansembe ochita zamatsenga a ku Iguputo anachitanso zomwezo mwa matsenga awo.+ Ekisodo 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo ansembe ochita zamatsenga sanathe kuonekera pamaso pa Mose chifukwa cha zithupsazo, popeza zinatuluka pa ansembewo ndi pa Aiguputo onse.+ Danieli 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pa nkhani iliyonse imene mfumu inali kufunsira nzeru kwa iwo kuti imvetse bwino,+ inaona kuti iwo anali anzeru kuwirikiza maulendo 10 kuposa ansembe onse ochita zamatsenga+ ndi anthu onse olankhula ndi mizimu+ amene anali mu ufumu wake. 2 Timoteyo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano monga mmene Yane ndi Yambure+ anatsutsira Mose, anthu amenewanso akupitiriza kutsutsa choonadi.+ Iwo ali ndi maganizo opotoka kwambiri,+ ndipo sakuyenerera chikhulupirirochi.+
11 Komabe, Farao nayenso anaitana amuna ake anzeru ndi amatsenga.+ Choncho ansembe ochita zamatsenga a ku Iguputo anachitanso zomwezo mwa matsenga awo.+
11 Ndipo ansembe ochita zamatsenga sanathe kuonekera pamaso pa Mose chifukwa cha zithupsazo, popeza zinatuluka pa ansembewo ndi pa Aiguputo onse.+
20 Pa nkhani iliyonse imene mfumu inali kufunsira nzeru kwa iwo kuti imvetse bwino,+ inaona kuti iwo anali anzeru kuwirikiza maulendo 10 kuposa ansembe onse ochita zamatsenga+ ndi anthu onse olankhula ndi mizimu+ amene anali mu ufumu wake.
8 Tsopano monga mmene Yane ndi Yambure+ anatsutsira Mose, anthu amenewanso akupitiriza kutsutsa choonadi.+ Iwo ali ndi maganizo opotoka kwambiri,+ ndipo sakuyenerera chikhulupirirochi.+