Salimo 119:100 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 100 Ndimachita zinthu mozindikira kuposa anthu achikulire,+Chifukwa ndimasunga malamulo anu.+ Miyambo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nzeru ndiyo chinthu chofunika kwambiri.+ Peza nzeru, ndipo pa zinthu zonse zimene upeze, upezenso luso lomvetsa zinthu.+ Miyambo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Uzilemekeze kwambiri ndipo zidzakukweza.+ Zidzakulemekeza chifukwa chakuti wazikumbatira.+
7 Nzeru ndiyo chinthu chofunika kwambiri.+ Peza nzeru, ndipo pa zinthu zonse zimene upeze, upezenso luso lomvetsa zinthu.+