Ekisodo 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako Farao anatumiza atumiki ake kukaitana Mose ndi Aroni ndi kuwauza kuti: “Tsopano ndachimwa.+ Yehova ndi wolungama,+ koma ine ndi anthu anga ndife olakwa. 1 Samueli 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Poyankha Sauli anati: “Ndachimwa.+ Bwerera mwana wanga Davide, pakuti sindidzakuvulaza chifukwa moyo wanga wakhala wamtengo wapatali+ kwa iwe lero. Taona, ndachita zinthu mopusa ndipo ndalakwitsa kwambiri.”
27 Kenako Farao anatumiza atumiki ake kukaitana Mose ndi Aroni ndi kuwauza kuti: “Tsopano ndachimwa.+ Yehova ndi wolungama,+ koma ine ndi anthu anga ndife olakwa.
21 Poyankha Sauli anati: “Ndachimwa.+ Bwerera mwana wanga Davide, pakuti sindidzakuvulaza chifukwa moyo wanga wakhala wamtengo wapatali+ kwa iwe lero. Taona, ndachita zinthu mopusa ndipo ndalakwitsa kwambiri.”