Ekisodo 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Zitatero anthuwo anakhulupirira+ Mose. Atamva kuti Yehova wacheukira+ ana a Isiraeli, ndi kutinso waona nsautso yawo,+ anagwada ndi kuweramira pansi.+ Nehemiya 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Ezara anatamanda Yehova+ Mulungu woona, Mulungu wamkulu. Atatero anthu onse anakweza manja awo m’mwamba+ ndi kuyankha kuti, “Ame! Ame!”*+ Ndiyeno anthuwo anagwada+ ndi kuwerama pamaso pa Yehova mpaka nkhope zawo pansi.+
31 Zitatero anthuwo anakhulupirira+ Mose. Atamva kuti Yehova wacheukira+ ana a Isiraeli, ndi kutinso waona nsautso yawo,+ anagwada ndi kuweramira pansi.+
6 Kenako Ezara anatamanda Yehova+ Mulungu woona, Mulungu wamkulu. Atatero anthu onse anakweza manja awo m’mwamba+ ndi kuyankha kuti, “Ame! Ame!”*+ Ndiyeno anthuwo anagwada+ ndi kuwerama pamaso pa Yehova mpaka nkhope zawo pansi.+