Salimo 148:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Onse, anthu ndi nyama, atamande dzina la Yehova,+Pakuti dzina lake lokhalo lili pamwamba posafikirika.+Ulemerero wake uli pamwamba kuposa dziko lapansi ndi kumwamba.+ Yesaya 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova wa makamu adzakwezeka kudzera m’chiweruzo,+ ndipo Mulungu woona, Woyera,+ adzadziyeretsa kudzera m’chilungamo.+ Yesaya 37:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+
13 Onse, anthu ndi nyama, atamande dzina la Yehova,+Pakuti dzina lake lokhalo lili pamwamba posafikirika.+Ulemerero wake uli pamwamba kuposa dziko lapansi ndi kumwamba.+
16 Yehova wa makamu adzakwezeka kudzera m’chiweruzo,+ ndipo Mulungu woona, Woyera,+ adzadziyeretsa kudzera m’chilungamo.+
23 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+