Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 18:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 ngati salandira chiwongoladzanja akabwereketsa zinthu,+ ndiponso sakongoza zinthu mwa katapira,*+ ngati sachita zopanda chilungamo,+ ngati amachita chilungamo chenicheni poweruza munthu ndi mnzake,+

  • Danieli 6:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Chotero amuna amphamvuwa anati: “Danieliyu sitingamupezere chifukwa chilichonse. Ngati tikufuna kumupezera chifukwa, chikhale chokhudzana ndi lamulo la Mulungu wake.”+

  • 1 Atesalonika 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Inu ndinu mboni, Mulungunso ndi mboni, za mmene tinakhalira okhulupirika, olungama, ndi opanda chifukwa chotinenezera,+ kwa inu okhulupirira.

  • 1 Timoteyo 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Komanso, akhale woti ngakhale anthu akunja* akumuchitira umboni wabwino,+ kuti asatonzedwe ndi kukodwa mumsampha+ wa Mdyerekezi.

  • Tito 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pakuti woyang’anira ayenera kukhala wopanda chifukwa chomunenezera.+ Pokhala mtumiki*+ wa Mulungu, asakhale womva zake zokha,+ wa mtima wapachala,+ womwa mowa mwauchidakwa,*+ wandewu,+ kapena wokonda kupeza phindu mwachinyengo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena