Ekisodo 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Mose anayankha Yehova kuti: “Komatu ana a Isiraeli sanandimvere,+ nanga Farao akandimvera bwanji?+ Pakuti ndimalankhula movutikira.”*+ 2 Samueli 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamenepo Mfumu Davide inabwera ndi kukhala pansi pamaso pa Yehova, ndipo inati: “Ndine yani ine,+ Yehova Ambuye Wamkulu Koposa? Ndipo nyumba yanga n’chiyani kuti mundifikitse pamene ndili pano? Yeremiya 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma ine ndinati: “Haa! Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ine sindingathe kulankhula+ chifukwa ndine mwana.”+
12 Koma Mose anayankha Yehova kuti: “Komatu ana a Isiraeli sanandimvere,+ nanga Farao akandimvera bwanji?+ Pakuti ndimalankhula movutikira.”*+
18 Pamenepo Mfumu Davide inabwera ndi kukhala pansi pamaso pa Yehova, ndipo inati: “Ndine yani ine,+ Yehova Ambuye Wamkulu Koposa? Ndipo nyumba yanga n’chiyani kuti mundifikitse pamene ndili pano?
6 Koma ine ndinati: “Haa! Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ine sindingathe kulankhula+ chifukwa ndine mwana.”+