2 Samueli 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako Tamara anadzithira phulusa+ kumutu ndi kung’amba malaya ake amizeremizere aja. Ndiyeno anaika manja ake pamutu+ n’kunyamuka kumapita, akulira. Ezara 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi yopereka nsembe yambewu+ yamadzulo, pambuyo podzichepetsa mwanjira imeneyi, ndinaimirira, zovala zanga zitang’ambika, ndipo ndinagwada+ n’kutambasulira manja anga kwa Yehova Mulungu wanga.+
19 Kenako Tamara anadzithira phulusa+ kumutu ndi kung’amba malaya ake amizeremizere aja. Ndiyeno anaika manja ake pamutu+ n’kunyamuka kumapita, akulira.
5 Pa nthawi yopereka nsembe yambewu+ yamadzulo, pambuyo podzichepetsa mwanjira imeneyi, ndinaimirira, zovala zanga zitang’ambika, ndipo ndinagwada+ n’kutambasulira manja anga kwa Yehova Mulungu wanga.+