Levitiko 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo wansembe azitentha+ zinthu zonsezi paguwa lansembe monga chakudya,+ kuti chikhale nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova. Levitiko 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Azikhala oyera kwa Mulungu wawo+ ndipo asaipitse dzina la Mulungu wawo,+ chifukwa iwowa amapereka nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova, mkate wa Mulungu wawo,+ choncho azikhala oyera.+ Numeri 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lamula ana a Isiraeli kuti, ‘Muzionetsetsa kuti pa nthawi yake yoikidwiratu+ mukupereka kwa ine nsembe yanga, yomwe ndi chakudya changa+ chotentha ndi moto, chotulutsa fungo londikhazika mtima pansi.’+
11 Ndipo wansembe azitentha+ zinthu zonsezi paguwa lansembe monga chakudya,+ kuti chikhale nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova.
6 Azikhala oyera kwa Mulungu wawo+ ndipo asaipitse dzina la Mulungu wawo,+ chifukwa iwowa amapereka nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova, mkate wa Mulungu wawo,+ choncho azikhala oyera.+
2 “Lamula ana a Isiraeli kuti, ‘Muzionetsetsa kuti pa nthawi yake yoikidwiratu+ mukupereka kwa ine nsembe yanga, yomwe ndi chakudya changa+ chotentha ndi moto, chotulutsa fungo londikhazika mtima pansi.’+