Numeri 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ngati bambo ake am’kaniza pa tsiku limene amva malonjezo ake onse, malonjezo ake odzimana amene walumbirira moyo wake, akhale opanda ntchito. Yehova adzam’khululukira chifukwa bambo ake anam’kaniza.+ Numeri 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mwamunayo akam’kaniza pa tsiku limene wamva kulonjezako,+ ndiye kuti wafafaniza lonjezo la mkaziyo, kapena lonjezo lake limene anachita mosaganizira bwino, limene analumbirira moyo wake ndi pakamwa pake. Yehova adzam’khululukira mkaziyo.+
5 Koma ngati bambo ake am’kaniza pa tsiku limene amva malonjezo ake onse, malonjezo ake odzimana amene walumbirira moyo wake, akhale opanda ntchito. Yehova adzam’khululukira chifukwa bambo ake anam’kaniza.+
8 Mwamunayo akam’kaniza pa tsiku limene wamva kulonjezako,+ ndiye kuti wafafaniza lonjezo la mkaziyo, kapena lonjezo lake limene anachita mosaganizira bwino, limene analumbirira moyo wake ndi pakamwa pake. Yehova adzam’khululukira mkaziyo.+