Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 18:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Aroni, kuti: “Inetu ndakupatsa udindo woyang’anira zopereka zonse zoperekedwa kwa ine.+ Pa zinthu zonse zopatulika zimene ana a Isiraeli azipereka, ndakupatsako gawo iweyo ndi ana ako, likhale gawo lanu mpaka kalekale.+

  • Numeri 18:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Zopereka zonse zopatulika,+ zimene ana a Isiraeli azipereka kwa Yehova, ndakupatsa iwe ndi ana ako aamuna ndi aakazi, ngati gawo lanu mpaka kalekale.+ Limeneli ndi pangano losatha* limene lidzakhala mpaka kalekale pakati pa Yehova ndi iwe ndi mbadwa zako.”+

  • 1 Akorinto 9:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Momwemonso, Ambuye anakonza+ kuti olengeza uthenga wabwino azipeza zodzisamalira pa moyo kudzera mwa uthenga wabwino.+

  • Agalatiya 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Komanso, aliyense amene akuphunzitsidwa mawuwo+ agawane+ zinthu zonse zabwino ndi amene akumuphunzitsayo.+

  • Aheberi 7:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Zoonadi, amuna ochokera mwa ana aamuna a Levi,+ amene amalandira udindo wa unsembe, amalamulidwa kulandira zakhumi+ kuchokera kwa anthu+ malinga ndi Chilamulo. Izi zikutanthauza kuti, amalandira zakhumizo kuchokera kwa abale awo, ngakhale kuti abale awowo anachokera m’chiuno mwa Abulahamu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena