Genesis 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuwonjezera pamenepo, ndidzafunsa za magazi anu. Ngati magazi anu akhetsedwa ndi chamoyo chilichonse, chamoyocho chiyenera kuphedwa, ndipo ngati moyo wa munthu wachotsedwa ndi munthu mnzake ndidzaufuna kuchokera kwa iye.+ Ekisodo 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munthu amene wapsera mtima mnzake mpaka kumupha mwachiwembu,+ ngakhale atathawira kuguwa langa lansembe kuti atetezeke, muzimuchotsa n’kukamupha.+ Deuteronomo 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Diso lako lisamumvere chisoni+ ndipo uzichotsa mlandu wa magazi a munthu wosalakwa mu Isiraeli+ kuti zinthu zikuyendere bwino.
5 Kuwonjezera pamenepo, ndidzafunsa za magazi anu. Ngati magazi anu akhetsedwa ndi chamoyo chilichonse, chamoyocho chiyenera kuphedwa, ndipo ngati moyo wa munthu wachotsedwa ndi munthu mnzake ndidzaufuna kuchokera kwa iye.+
14 Munthu amene wapsera mtima mnzake mpaka kumupha mwachiwembu,+ ngakhale atathawira kuguwa langa lansembe kuti atetezeke, muzimuchotsa n’kukamupha.+
13 Diso lako lisamumvere chisoni+ ndipo uzichotsa mlandu wa magazi a munthu wosalakwa mu Isiraeli+ kuti zinthu zikuyendere bwino.