Levitiko 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Munthu wochita chigololo ndi mkazi wa munthu wina, wachita chigololo ndi mkazi wa mnzake.+ Mwamuna ndi mkazi amene achita chigololowo aziphedwa ndithu.+ 1 Atesalonika 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma akufuna kuti pasapezeke wina wopweteka m’bale wake kapena womuphwanyira ufulu wake pa nkhani imeneyi,+ chifukwa Yehova adzalanga anthu onse ochita zimenezi,+ monga mmene tinakuuzirani kale ndi kukufotokozerani momveka bwino.+ Aheberi 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ukwati ukhale wolemekezeka kwa onse, ndipo pogona pa anthu okwatirana pakhale posaipitsidwa,+ pakuti Mulungu adzaweruza adama ndi achigololo.+
10 “‘Munthu wochita chigololo ndi mkazi wa munthu wina, wachita chigololo ndi mkazi wa mnzake.+ Mwamuna ndi mkazi amene achita chigololowo aziphedwa ndithu.+
6 Koma akufuna kuti pasapezeke wina wopweteka m’bale wake kapena womuphwanyira ufulu wake pa nkhani imeneyi,+ chifukwa Yehova adzalanga anthu onse ochita zimenezi,+ monga mmene tinakuuzirani kale ndi kukufotokozerani momveka bwino.+
4 Ukwati ukhale wolemekezeka kwa onse, ndipo pogona pa anthu okwatirana pakhale posaipitsidwa,+ pakuti Mulungu adzaweruza adama ndi achigololo.+