Levitiko 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Muzisunga malangizo anga ndi zigamulo zanga. Mukatero mudzakhala otetezeka m’dzikolo.+ Deuteronomo 4:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Chilamulocho ndicho maumboni,*+ malangizo+ ndi zigamulo+ zimene Mose anauza ana a Isiraeli pamene anatuluka mu Iguputo. Salimo 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuopa+ Yehova n’koyera, ndipo kudzakhalapo kwamuyaya.Zigamulo+ za Yehova n’zolondola,+ ndipo pa mbali iliyonse zasonyezadi kuti ndi zolungama.+
45 Chilamulocho ndicho maumboni,*+ malangizo+ ndi zigamulo+ zimene Mose anauza ana a Isiraeli pamene anatuluka mu Iguputo.
9 Kuopa+ Yehova n’koyera, ndipo kudzakhalapo kwamuyaya.Zigamulo+ za Yehova n’zolondola,+ ndipo pa mbali iliyonse zasonyezadi kuti ndi zolungama.+