Oweruza 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo Yehova anayankha kuti: “Fuko la Yuda ndilo lidzayamba kupita.+ Ndipo ndidzaperekadi dzikolo m’manja mwawo.” 2 Samueli 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno pamene mfumu inali kukhala m’nyumba yake,+ ndipo Yehova ataipatsa mpumulo kwa adani ake onse oizungulira,+ 2 Samueli 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ine ndidzakhala ndi iwe kulikonse kumene udzapite,+ ndipo ndidzawononga ndi kuchotsa adani ako onse pamaso pako.+ Ndidzakupangira dzina lotchuka,+ lofanana ndi dzina la anthu otchuka amene ali m’dziko.
2 Pamenepo Yehova anayankha kuti: “Fuko la Yuda ndilo lidzayamba kupita.+ Ndipo ndidzaperekadi dzikolo m’manja mwawo.”
7 Ndiyeno pamene mfumu inali kukhala m’nyumba yake,+ ndipo Yehova ataipatsa mpumulo kwa adani ake onse oizungulira,+
9 Ine ndidzakhala ndi iwe kulikonse kumene udzapite,+ ndipo ndidzawononga ndi kuchotsa adani ako onse pamaso pako.+ Ndidzakupangira dzina lotchuka,+ lofanana ndi dzina la anthu otchuka amene ali m’dziko.