Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Yehova ndi Wopereka Umphawi+ ndi Wolemeretsa,+

      Wotsitsa ndiponso Wokweza,+

  • 1 Mbiri 14:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Davide anadziwa kuti Yehova wachititsa kuti ufumu wake ukhazikike+ mu Isiraeli, pakuti ufumu wake unakwezedwa kwambiri chifukwa cha anthu ake Aisiraeli.+

  • 1 Mbiri 14:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chotero Davide anatchuka+ mpaka mbiri yake inamveka kumayiko onse. Ndipo Yehova anachititsa kuti mitundu yonse iziopa Davide.+

  • 1 Mbiri 17:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ine ndidzakhala ndi iwe kulikonse kumene udzapite,+ ndipo ndidzawononga ndi kuchotsa adani ako onse+ pamaso pako. Ndidzakupangira dzina+ lofanana ndi dzina la anthu otchuka amene ali padziko lapansi.+

  • Mlaliki 7:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mbiri yabwino imaposa mafuta onunkhira,+ ndipo tsiku lomwalira limaposa tsiku lobadwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena