1 Mafumu 4:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndipo anthu ankabwera kuchokera ku mitundu yonse kudzamva nzeru za Solomo,+ ngakhalenso kuchokera kwa mafumu onse a padziko lapansi amene anamva za nzeru zake.+ 1 Mafumu 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Sindinakhulupirire mawuwo mpaka pamene ndabwera n’kuona ndi maso anga, ndipo ndaona kuti ndinangouzidwa hafu chabe.+ Nzeru zanu ndi ulemerero wanu zaposa zinthu zimene ndinamva.+ Danieli 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pa nkhani iliyonse imene mfumu inali kufunsira nzeru kwa iwo kuti imvetse bwino,+ inaona kuti iwo anali anzeru kuwirikiza maulendo 10 kuposa ansembe onse ochita zamatsenga+ ndi anthu onse olankhula ndi mizimu+ amene anali mu ufumu wake.
34 Ndipo anthu ankabwera kuchokera ku mitundu yonse kudzamva nzeru za Solomo,+ ngakhalenso kuchokera kwa mafumu onse a padziko lapansi amene anamva za nzeru zake.+
7 Sindinakhulupirire mawuwo mpaka pamene ndabwera n’kuona ndi maso anga, ndipo ndaona kuti ndinangouzidwa hafu chabe.+ Nzeru zanu ndi ulemerero wanu zaposa zinthu zimene ndinamva.+
20 Pa nkhani iliyonse imene mfumu inali kufunsira nzeru kwa iwo kuti imvetse bwino,+ inaona kuti iwo anali anzeru kuwirikiza maulendo 10 kuposa ansembe onse ochita zamatsenga+ ndi anthu onse olankhula ndi mizimu+ amene anali mu ufumu wake.