Numeri 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pambuyo pake Yehova anauza Mose ndi Aroni kuti: “Chifukwa simunasonyeze chikhulupiriro mwa ine, polephera kundilemekeza+ pamaso pa ana a Isiraeli, simudzaulowetsa mpingowu m’dziko limene ndidzawapatse.”+ Numeri 27:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pambuyo poliona dzikolo, udzaikidwa m’manda kuti ukagone ndi makolo ako.+ Ndithudi, iweyo udzaikidwa m’manda mofanana ndi Aroni m’bale wako,+ Deuteronomo 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo Yehova anapitiriza kundikwiyira chifukwa cha inu,+ ndipo sanandimvere. Motero Yehova anandiuza kuti, ‘Basi khala chete! Usatchulenso nkhani imeneyi kwa ine. Salimo 106:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kuwonjezera pamenepo, iwo anaputa mkwiyo pa madzi a ku Meriba,+Moti Mose sizinamuyendere bwino chifukwa cha anthu amenewa.+
12 Pambuyo pake Yehova anauza Mose ndi Aroni kuti: “Chifukwa simunasonyeze chikhulupiriro mwa ine, polephera kundilemekeza+ pamaso pa ana a Isiraeli, simudzaulowetsa mpingowu m’dziko limene ndidzawapatse.”+
13 Pambuyo poliona dzikolo, udzaikidwa m’manda kuti ukagone ndi makolo ako.+ Ndithudi, iweyo udzaikidwa m’manda mofanana ndi Aroni m’bale wako,+
26 Pamenepo Yehova anapitiriza kundikwiyira chifukwa cha inu,+ ndipo sanandimvere. Motero Yehova anandiuza kuti, ‘Basi khala chete! Usatchulenso nkhani imeneyi kwa ine.
32 Kuwonjezera pamenepo, iwo anaputa mkwiyo pa madzi a ku Meriba,+Moti Mose sizinamuyendere bwino chifukwa cha anthu amenewa.+