Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 33:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pamenepo Mulungu anati: “Ineyo ndidzayenda nawe+ ndipo ndidzakupatsa mpumulo.”+

  • Yoswa 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Mukumbukire mawu amene Mose mtumiki wa Yehova anakulamulani,+ akuti, ‘Yehova Mulungu wanu akukupatsani mpumulo, ndipo wakupatsani dziko ili.

  • Yoswa 11:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Chotero Yoswa analanda dziko lonse monga mmene Yehova analonjezera Mose.+ Ndiyeno Yoswa anapereka dzikolo kwa Aisiraeli monga cholowa chawo, malinga ndi magawo awo potsata mafuko awo.+ Ndipo dziko lonse linakhala bata, lopanda nkhondo.+

  • Yoswa 22:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Tsopano Yehova Mulungu wanu wapatsa abale anu mpumulo monga momwe anawalonjezera.+ Chotero bwererani, mupite kumahema anu m’dziko lanu, limene Mose mtumiki wa Yehova anakupatsani kutsidya lina la Yorodano.+

  • Miyambo 16:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Yehova akasangalala ndi njira za munthu,+ amachititsa ngakhale adani a munthuyo kukhala naye pa mtendere.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena