Numeri 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Amenewa ndiwo osankhidwa a khamu la anthuwo, atsogoleri a mafuko+ a makolo awo. Aliyense wa iwo ndi mtsogoleri wa anthu masauzande mu Isiraeli.”+ Deuteronomo 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Sankhani amuna anzeru, aluso+ ndi ozindikira+ m’mafuko anu, kuti ndiwaike kukhala atsogoleri anu.’+ Yoswa 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Limeneli ndilo dziko limene ana a Isiraeli anatenga monga cholowa chawo m’dziko la Kanani.+ Wansembe Eleazara, Yoswa mwana wa Nuni, ndi atsogoleri a mafuko a makolo a ana a Isiraeli, ndiwo anagawa dzikolo kuti likhale cholowa chawo.+ Yoswa 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Atamva zimenezi, ana a Rubeni, ana a Gadi, ndi hafu ya fuko la Manase anayankha+ atsogoleri a masauzande a Aisiraeli, kuti:+
16 Amenewa ndiwo osankhidwa a khamu la anthuwo, atsogoleri a mafuko+ a makolo awo. Aliyense wa iwo ndi mtsogoleri wa anthu masauzande mu Isiraeli.”+
13 Sankhani amuna anzeru, aluso+ ndi ozindikira+ m’mafuko anu, kuti ndiwaike kukhala atsogoleri anu.’+
14 Limeneli ndilo dziko limene ana a Isiraeli anatenga monga cholowa chawo m’dziko la Kanani.+ Wansembe Eleazara, Yoswa mwana wa Nuni, ndi atsogoleri a mafuko a makolo a ana a Isiraeli, ndiwo anagawa dzikolo kuti likhale cholowa chawo.+
21 Atamva zimenezi, ana a Rubeni, ana a Gadi, ndi hafu ya fuko la Manase anayankha+ atsogoleri a masauzande a Aisiraeli, kuti:+