Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 18:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Atakweza maso,+ anaona amuna atatu ataima chapatali ndi iye. Atawaona, ananyamuka pakhomo la hemayo n’kuthamanga kukakumana nawo. Atafika, anagwada n’kuwaweramira mpaka nkhope yake pansi.+

  • Ekisodo 23:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pakuti mngelo wanga adzakutsogolera ndi kukulowetsa m’dziko la Aamori, Ahiti, Aperezi, Akanani, Ahivi ndi Ayebusi, ndipo ndidzawafafaniza ndithu.+

  • Oweruza 13:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kenako mkaziyo anapita kukauza mwamuna wake kuti: “Munthu wa Mulungu woona anabwera kwa ine, ndipo maonekedwe ake anali ofanana ndi mngelo wa Mulungu woona,+ maonekedwe ochititsa mantha kwambiri.+ Koma sindinam’funse kumene wachokera ndiponso sanandiuze dzina lake.+

  • Machitidwe 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mmene iwo anali kuyang’anitsitsa kuthambo pamene iye anali kukwera kumwamba,+ panaonekera amuna awiri ovala zoyera+ ataimirira pambali pawo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena