Genesis 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno anati: “Chonde ambuyanga, patukirani kunyumba ya kapolo wanu. Tikusambitseni mapazi ndiponso mukagone,+ kuti mawa mulawirire n’kupitiriza ulendo wanu.”+ Ndiyeno iwo anati: “Ayi, ife tigona m’bwalo la mzinda usiku wa lero.”+ Oweruza 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma mwamuna wokalamba uja anati: “Mtendere ukhale nawe!+ Ine ndidzakupatsa chilichonse chimene ungafunikire.+ Koma usagone pabwalo la mzinda.” Yesaya 58:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndimafunanso kuti muzigawira chakudya chanu anthu anjala,+ ndiponso kuti muziitanira m’nyumba zanu anthu osautsika ndi osowa pokhala.+ Ndimafuna kuti mukaona munthu wosavala muzimuveka+ ndiponso kuti musamadzibise kwa abale anu.+
2 Ndiyeno anati: “Chonde ambuyanga, patukirani kunyumba ya kapolo wanu. Tikusambitseni mapazi ndiponso mukagone,+ kuti mawa mulawirire n’kupitiriza ulendo wanu.”+ Ndiyeno iwo anati: “Ayi, ife tigona m’bwalo la mzinda usiku wa lero.”+
20 Koma mwamuna wokalamba uja anati: “Mtendere ukhale nawe!+ Ine ndidzakupatsa chilichonse chimene ungafunikire.+ Koma usagone pabwalo la mzinda.”
7 Ndimafunanso kuti muzigawira chakudya chanu anthu anjala,+ ndiponso kuti muziitanira m’nyumba zanu anthu osautsika ndi osowa pokhala.+ Ndimafuna kuti mukaona munthu wosavala muzimuveka+ ndiponso kuti musamadzibise kwa abale anu.+