Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 19:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Choncho anakhala pansi ndipo onse awiri anayamba kudya ndi kumwera pamodzi. Kenako bambo a mtsikanayo anauza mwamunayo kuti: “Chonde, lero mugone, mupite mawa,+ ndipo musangalatse mtima wanu.”+

  • Oweruza 19:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Tsopano mwamunayo+ anaimirira kuti azipita, iyeyo pamodzi ndi mdzakazi wake+ ndiponso mtumiki wake,+ koma apongozi ake, bambo a mtsikanayo, anamuuza kuti: “Anotu ndi madzulo tsopano, ndipo posachedwa kuchita mdima. Chonde, lero mugone kuno.+ Onani, kunja kwatsala pang’ono kuda. Lero mugone kuno ndipo musangalatse mtima wanu.+ Mawa mudzuke m’mawa kwambiri ndi kuyamba ulendo wanu wopita kuhema wanu.”

  • Salimo 104:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Komanso kuti mutuluke vinyo amene amasangalatsa mtima wa munthu.+

      Amachita zonsezi kuti nkhope ya munthu isalale ndi mafuta,+

      Komanso kuti apereke chakudya chimene chimakhutiritsa mtima wa munthu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena