1 Samueli 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Munthu akachimwira mnzake,+ Mulungu adzam’pepesera,+ koma kodi akachimwira Yehova,+ angamupempherere ndani?”+ Koma anawo sanali kumvera bambo awo+ chifukwa tsopano Yehova anali atatsimikiza mtima kuti awaphe.+ Miyambo 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Munthu wodzudzulidwa kawirikawiri+ koma amene amaumitsa khosi lake,+ adzathyoledwa mwadzidzidzi ndipo akadzatero sadzachira.+ Hoseya 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aisiraeli azama nazo zinthu zowononga+ ngati m’masiku a Gibeya.+ Mulungu adzakumbukira zolakwa zawo+ ndipo adzawalanga chifukwa cha machimo awo. Hoseya 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Inu ana a Isiraeli, mwakhala mukuchimwa kuyambira m’masiku a Gibeya+ ndipo anthu anapitirizabe kuchita machimo kumeneko. Nkhondo ya ku Gibeya yomenyana ndi anthu osalungama sinawawononge onse.+ Aroma 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chotero, iye amachitira chifundo munthu amene wafuna kumuchitira chifundo,+ koma amalola anthu ena kuti aumitse mitima yawo.+
25 Munthu akachimwira mnzake,+ Mulungu adzam’pepesera,+ koma kodi akachimwira Yehova,+ angamupempherere ndani?”+ Koma anawo sanali kumvera bambo awo+ chifukwa tsopano Yehova anali atatsimikiza mtima kuti awaphe.+
29 Munthu wodzudzulidwa kawirikawiri+ koma amene amaumitsa khosi lake,+ adzathyoledwa mwadzidzidzi ndipo akadzatero sadzachira.+
9 Aisiraeli azama nazo zinthu zowononga+ ngati m’masiku a Gibeya.+ Mulungu adzakumbukira zolakwa zawo+ ndipo adzawalanga chifukwa cha machimo awo.
9 “Inu ana a Isiraeli, mwakhala mukuchimwa kuyambira m’masiku a Gibeya+ ndipo anthu anapitirizabe kuchita machimo kumeneko. Nkhondo ya ku Gibeya yomenyana ndi anthu osalungama sinawawononge onse.+
18 Chotero, iye amachitira chifundo munthu amene wafuna kumuchitira chifundo,+ koma amalola anthu ena kuti aumitse mitima yawo.+