Deuteronomo 32:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kubwezera ndi kwanga, chilangonso ndi changa.+Pa nthawi yoikidwiratu phazi lawo lidzaterereka poyenda,+Pakuti tsiku la tsoka lawo layandikira,+Ndipo zowagwera zikufika mofulumira.’+ 1 Samueli 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma Samueli anati: “Monga mmene akazi anaferedwera ana awo chifukwa cha lupanga lako,+ momwemonso mayi ako+ aferedwa ana koposa akazi onse.”+ Pamenepo Samueli anadula Agagi nthulinthuli pamaso pa Yehova ku Giligala.+ Esitere 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma Esitere ataonekera pamaso pa mfumu, mfumuyo inalemba lamulo lakuti:+ “Chiwembu+ chake choipa chimene anakonzera Ayuda chimugwere iyeyo.”+ Choncho Hamani komanso ana ake anawapachika pamtengo.+
35 Kubwezera ndi kwanga, chilangonso ndi changa.+Pa nthawi yoikidwiratu phazi lawo lidzaterereka poyenda,+Pakuti tsiku la tsoka lawo layandikira,+Ndipo zowagwera zikufika mofulumira.’+
33 Koma Samueli anati: “Monga mmene akazi anaferedwera ana awo chifukwa cha lupanga lako,+ momwemonso mayi ako+ aferedwa ana koposa akazi onse.”+ Pamenepo Samueli anadula Agagi nthulinthuli pamaso pa Yehova ku Giligala.+
25 Koma Esitere ataonekera pamaso pa mfumu, mfumuyo inalemba lamulo lakuti:+ “Chiwembu+ chake choipa chimene anakonzera Ayuda chimugwere iyeyo.”+ Choncho Hamani komanso ana ake anawapachika pamtengo.+