Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 21:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Choncho Aisiraeli analanda mizinda yonseyi n’kuyamba kukhala m’mizinda yonse ya Aamori+ ku Hesiboni,+ ndi m’midzi yake yonse yozungulira.

  • Deuteronomo 2:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 “‘Nyamukani, muyende ndi kudutsa chigwa cha Arinoni.+ Taonani, ndapereka m’manja mwanu Sihoni,+ Mwamori, mfumu ya Hesiboni. Yambani kulanda dziko lake, ndipo menyanani naye nkhondo.

  • Deuteronomo 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Chotero Yehova anandiuza kuti, ‘Usamuope ameneyu,+ chifukwa ndim’pereka ndithu m’manja mwako. Ndim’pereka pamodzi ndi anthu ake onse ndi dziko lake. Umuchite zimene unachitira Sihoni+ mfumu ya Aamori, amene anali kukhala m’Hesiboni.’

  • Yoswa 12:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Sihoni+ mfumu ya Aamori, yemwe ankakhala ku Hesiboni.+ Dera lomwe anali kulamulira linkayambira pakatikati pa chigwa cha Arinoni kuphatikizapo mzinda wa Aroweli,+ umene unali m’mphepete mwa mtsinje wa Arinoni,+ mpaka hafu ya Giliyadi kukalekezera kuchigwa cha Yaboki,+ kumalire ndi ana a Amoni.

  • Yoswa 13:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Anawapatsanso mizinda yonse ya Sihoni mfumu ya Aamori imene inali kulamulira ku Hesiboni, mpaka kumalire ndi ana a Amoni.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena