Mlaliki 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mapeto a chinthu amakhala bwino kuposa chiyambi chake,+ ndipo munthu woleza mtima ndi wabwino kuposa munthu wodzikuza.+ Mika 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwe mdani wanga,+ usasangalale chifukwa cha zimene zandichitikira. Ngakhale kuti ndagwa, ndidzadzuka ndithu.+ Ngakhale kuti ndili mumdima,+ Yehova adzakhala kuwala kwanga.+
8 Mapeto a chinthu amakhala bwino kuposa chiyambi chake,+ ndipo munthu woleza mtima ndi wabwino kuposa munthu wodzikuza.+
8 Iwe mdani wanga,+ usasangalale chifukwa cha zimene zandichitikira. Ngakhale kuti ndagwa, ndidzadzuka ndithu.+ Ngakhale kuti ndili mumdima,+ Yehova adzakhala kuwala kwanga.+