Yoswa 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano Yoswa anali atakalamba, ndipo anali ndi zaka zambiri.+ Choncho Yehova anamuuza kuti: “Iweyo wakalamba ndipo uli ndi zaka zambiri, koma dziko loti lilandidwe likadali lalikulu.+ Yoswa 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Dziko limene latsala ndi ili:+ Madera onse a Afilisiti+ ndi madera onse a Agesuri.+ Oweruza 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Bambo ndi mayi a Samisoni sanadziwe kuti Yehova ndi amene anali kuchititsa zimenezi.+ Iwo sanadziwe kuti anali kufunafuna mpata woti amenyane ndi Afilisiti, chifukwa pa nthawiyi Afilisiti anali kulamulira Isiraeli.+
13 Tsopano Yoswa anali atakalamba, ndipo anali ndi zaka zambiri.+ Choncho Yehova anamuuza kuti: “Iweyo wakalamba ndipo uli ndi zaka zambiri, koma dziko loti lilandidwe likadali lalikulu.+
4 Bambo ndi mayi a Samisoni sanadziwe kuti Yehova ndi amene anali kuchititsa zimenezi.+ Iwo sanadziwe kuti anali kufunafuna mpata woti amenyane ndi Afilisiti, chifukwa pa nthawiyi Afilisiti anali kulamulira Isiraeli.+