Deuteronomo 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Musakachite zimene tikuchita kuno lero, aliyense kumangochita zimene akufuna,+ Deuteronomo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Ukamveradi mawu a Yehova Mulungu wako mwa kuonetsetsa kuti ukutsatira malamulo ake onse amene ndikukupatsa lero,+ Yehova Mulungu wako adzakukweza ndithu pamwamba pa mitundu yonse ya padziko lapansi.+ Oweruza 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Masiku amenewo mu Isiraeli munalibe mfumu.+ Aliyense anali kuchita zimene anali kuona kuti n’zoyenera.+ Miyambo 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pali njira yooneka ngati yowongoka kwa munthu,+ koma mapeto ake ndi imfa.+ Miyambo 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Njira zonse za munthu zimaoneka zoyera m’maganizo mwake,+ koma Yehova amafufuza zolinga zake.+ Miyambo 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Njira iliyonse ya munthu imaoneka yowongoka m’maganizo mwake,+ koma Yehova amafufuza mitima.+
28 “Ukamveradi mawu a Yehova Mulungu wako mwa kuonetsetsa kuti ukutsatira malamulo ake onse amene ndikukupatsa lero,+ Yehova Mulungu wako adzakukweza ndithu pamwamba pa mitundu yonse ya padziko lapansi.+
25 Masiku amenewo mu Isiraeli munalibe mfumu.+ Aliyense anali kuchita zimene anali kuona kuti n’zoyenera.+