Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 43:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Iwo anayankha kuti: “Kapolo wanu bambo athu ali bwino. Adakali ndi moyo.” Atatero anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi.+

  • 1 Samueli 24:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pambuyo pake, Davide nayenso anatuluka m’phangamo ndi kuitana Sauli kuti: “Mbuyanga+ mfumu!” Pamenepo Sauli anacheuka ndipo Davide anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi.+

  • 1 Samueli 25:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Abigayeli ataona Davide, nthawi yomweyo anatsika mofulumira pabulu wake. Iye anagwada pamaso pa Davide ndi kuwerama mpaka nkhope yake pansi.+

  • 2 Samueli 9:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Mefiboseti mwana wa Yonatani, mwana wa Sauli, atalowa ndi kuonana ndi Davide, nthawi yomweyo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi.+ Pamenepo Davide anati: “Mefiboseti!” Poyankha, iye anati: “Ndine pano mtumiki wanu.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena