1 Samueli 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako amuna a ku Zifi+ anapita kwa Sauli ku Gibeya+ kukamuuza kuti: “Kodi Davide si uyu akubisala+ pafupi ndi ife m’malo ovuta kufikamo ku Horesi,+ paphiri la Hakila+ limene lili kudzanja lamanja* la Yesimoni?*+
19 Kenako amuna a ku Zifi+ anapita kwa Sauli ku Gibeya+ kukamuuza kuti: “Kodi Davide si uyu akubisala+ pafupi ndi ife m’malo ovuta kufikamo ku Horesi,+ paphiri la Hakila+ limene lili kudzanja lamanja* la Yesimoni?*+