Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 22:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pamenepo mfumu inauza asilikali othamanga+ amene anaima pamaso pake kuti: “Tembenukani ndi kupha ansembe a Yehova chifukwa ali kumbali ya Davide. Iwo anali kudziwanso kuti Davide ndi wothawa koma sanaulule kwa ine!”+ Koma atumiki a mfumuwo sanafune kutambasula manja awo kuti akanthe ansembe a Yehova.+

  • 1 Samueli 26:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Patapita nthawi, amuna a ku Zifi+ anapita kwa Sauli ku Gibeya,+ ndipo anamuuza kuti: “Kodi simukudziwa kuti Davide akubisala kuphiri la Hakila+ moyang’anana ndi Yesimoni?”*+

  • Salimo 54:kam
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • Kwa wotsogolera nyimbo: Nyimboyi iimbidwe ndi zipangizo za zingwe. Masikili.* Salimo la Davide. Pa nthawi imene Zifi anabwera kudzauza Sauli kuti: “Kodi simukudziwa kuti Davide akubisala kwathu?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena