Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 25:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndipo mundipangire malo opatulika, popeza ndiyenera kukhala pakati panu.+

  • Ekisodo 40:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Mwezi woyamba, pa tsiku loyamba la mweziwo,+ udzautse chihema chopatulika, kapena kuti chihema chokumanako.+

  • 1 Samueli 1:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Mwanayo atangosiya kuyamwa, Hana anapita naye ku Silo atatenga ng’ombe yaing’ono yamphongo yazaka zitatu, ufa wokwana muyezo umodzi wa efa* ndi mtsuko waukulu wa vinyo.+ Iye analowa m’nyumba ya Yehova ku Silo,+ ndipo mwanayo anali naye limodzi.

  • 1 Samueli 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Nyale ya Mulungu inali isanazimitsidwe, ndipo Samueli anali atagona m’kachisi+ wa Yehova, mmene munali likasa la Mulungu.

  • 2 Samueli 7:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 inauza Natani+ mneneri kuti: “Tsopano taona, ine ndikukhala m’nyumba ya mitengo ya mkungudza,+ pamene likasa la Mulungu woona likukhala m’chihema chansalu.”+

  • 2 Samueli 22:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Pa nthawi ya zowawa zanga ndinaitana Yehova,+

      Ndinaitana Mulungu wanga.+

      Pamenepo iye anamva mawu anga ali m’kachisi wake,+

      Makutu ake anamva kulira kwanga kopempha thandizo.+

  • Salimo 27:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Chinthu chimodzi chimene ndapempha kwa Yehova,+

      Chimenecho ndi chimene ndimachikhumba,+

      N’chakuti, ndikhale m’nyumba ya Yehova masiku onse a moyo wanga,+

      Kuti ndione ubwino wa Yehova,+

      Komanso kuti ndiyang’ane kachisi wake moyamikira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena